1 Samueli 13:7 BL92

7 Ndipo Ahebri ena anaoloka Yordano nafika ku dziko la Gadi ndi Gileadi; koma Sauli akali ku Giligala, ndipo anthu onse anamtsata ndi kunthunthumira.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:7 nkhani