1 Samueli 13:8 BL92

8 Ndipo iye anatsotsa masiku asanu ndi awiri, monga nthawi anampanga Samueli; koma Samueli sanafika ku Giligala, ndipo anthu anabalalika namsiya Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:8 nkhani