1 Samueli 14:1 BL92

1 Ndipo kunali tsiku lina kuti Jonatani mwana wa Sauli ananena ndi mnyamata wonyamula zida zace, Tiye tipite kunka ku kaboma ka Afilisti, tsidya lija. Koma sanauza atate wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:1 nkhani