1 Samueli 14:13 BL92

13 Ndipo Jonatani anakwera cokwawa, ndi wonyamula zida zace anamtsata; ndi Afilisti anagwa pamaso pa Jonatani, ndi wonyamula zida zace anawapha pambuyo pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:13 nkhani