1 Samueli 14:14 BL92

14 Kuwapha koyambako, Jonatani ndi wonyamula zida zace, anapha monga anthu makumi awiri, monga ndime ya munda yolima ng'ombe ziwiri tsiku limodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:14 nkhani