1 Samueli 14:15 BL92

15 Ndipo kunali kunthunthumira kuzithando, kuthengoko, ndi pakati pa anthu onse; a ku kaboma ndi owawanya omwe ananthunthumira; ndi dziko linagwedezeka; comweco kunali kunthunthumira kwakukuru koposa,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:15 nkhani