1 Samueli 14:21 BL92

21 Ndiponso Ahebri akukhala nao Afilisti kale, amene anaturuka m'dziko lozungulira kukaiowa nao kuzithando; iwonso anatembenukira kuti akakhale ndi Aisrayeli amene anali ndi Sauli ndi Jonatani.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:21 nkhani