1 Samueli 14:22 BL92

22 Anateronso Aisrayeli onse akubisala m'phiri la Efraimu, pakumva kuti Afilisti anathawa, iwo anawapitikitsa kolimba kunkhondoko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:22 nkhani