1 Samueli 14:26 BL92

26 Ndipo pakufika anthuwo m'nkhalangomo, onani, madzi a uci anacuruka; koma panalibe munthu mmodzi anaika dzanja lace pakamwa, pakuti anthuwo anaopa tembererolo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:26 nkhani