1 Samueli 14:32 BL92

32 Ndipo anthuwo anathamangira zowawanyazo, natenga nkhosa, ndi ng'ombe, ndi ana a ng'ombe, naziphera pansi; anthu nazidya ziri ndi mwazi wao.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:32 nkhani