1 Samueli 14:33 BL92

33 Pamenepo anauza Sauli, kuti, Onani anthu alikucimwira Yehova, umo akudya zamwazi. Ndipo iye anati, Munacita konyenga; kunkhunizani mwala waukuru kwa ine lero.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:33 nkhani