1 Samueli 15:1 BL92

1 Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ace Aisrayeli; cifukwa cace tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:1 nkhani