1 Samueli 15:12 BL92

12 Ndipo Samueli analawirira m'mawa kuti akakomane ndi Sauli; ndipo munthu anamuuza Samueli kuti, Sauli anafika ku Karimeli, ndipo taonani, anaimika cikumbutso cace, nazungulira, napitirira, natsikira ku Giligala.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:12 nkhani