1 Samueli 15:13 BL92

13 Ndipo Samueli anadza kwa Sauli; ndipo Sauli anati kwa iye, Yehova akudalitseni; ine ndinacita lamulo la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:13 nkhani