1 Samueli 15:16 BL92

16 Pomwepo Samueli ananena ndi Sauli, Imani, ndidzakudziwitsani cimene Yehova wanena ndi ine usiku walero. Ndipo iyeyo anati kwa iye, Nenani.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:16 nkhani