1 Samueli 15:30 BL92

30 Pomwepo iye anati, Ndinacimwa, koma mundicitire ulemu tsopano pamaso pa akuru a anthu anga, ndi pamaso pa Israyeli, nimubwerere pamodzi ndi ine, kuti ndikalambire Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:30 nkhani