32 Ndipo Samueli anati, Bwerani naye kwa ine kuno Agagi mfumu ya Aamaleki. Ndipo Agagi anabwera kwa iye mokondwera. Nati Agagi, Zoonadi kuwawa kwa imfa kunapitirira.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15
Onani 1 Samueli 15:32 nkhani