1 Samueli 15:8 BL92

8 Namtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleki, naononga konse konse anthu onse ndi lupanga lakuthwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:8 nkhani