1 Samueli 17:17 BL92

17 Ndipo Jese anati kwa Davide mwana wace, Uwatengere abale ako efa watirigu uyu wokazinga, ndi mikate iyi khumi, nuthamangire nazo kuzithando kwa abale ako;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:17 nkhani