1 Samueli 17:34 BL92

34 Ndipo Davide anati kwa Sauli, Ine kapolo wanu ndinalikusunga nkhosa za atate wanga; ndipo pakubwera mkango, mwina cimbalangondo ndi kutenga nkhosa ya gululo,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:34 nkhani