1 Samueli 17:35 BL92

35 ndinacithamangira, ndi kucikantha, ndi kuiturutsa m'kamwa mwace; ndipo pamene cinaneliukira, ndinagwira cowa lace ndi kucikantha ndi kucipha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:35 nkhani