1 Samueli 17:36 BL92

36 Ine kapolo wanu ndinapha mkango ndi cimbalangondo zonse ziwiri; ndipo Mfilisti uyu wosadulidwa adzakhala ngati mmodzi wa izo, popeza wanyoza makamu a Mulungu wamoyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:36 nkhani