1 Samueli 17:39 BL92

39 Ndipo Davide anamanga lupanga lace pamwamba pa zobvala zace, nayesa kuyenda nazo; popeza sanaziyesera kale. Ndipo Davide anati kwa Sauli, Sindikhoza kuyenda ndi izi; pakuti sindinazizolowera. Nazibvula Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:39 nkhani