1 Samueli 17:40 BL92

40 Natenga ndodo yace m'dzanja lace nadzisankhira miyala isanu yosalala ya mumtsinje, naiika m'thumba la kubusa, limene anali nalo ndilo cibete; ndi coponyera miyala cinali m'dzanja lace, momwemo anayandikira kwa Mfilistiyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:40 nkhani