1 Samueli 17:47 BL92

47 Ndi msonkhano wonse uno udzazindikira kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga, kapena ndi mkondo; pakuti Yehova ndiye mwini nkhondo, ndipo iye adzakuperekani inu m'manja athu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:47 nkhani