1 Samueli 17:48 BL92

48 Ndipo kunali, pamene Mfilistiyo anadzikonza, nadza, nasendera pafupi kuti akomane ndi Davide, Davide anafulumira, nathamangira ku khamulo, kuti akomane ndi Mfilistiyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:48 nkhani