8 Naima iye naitana makamu a nkhondo a Israyeli, nanena nao, Munaturukiranji kundandalitsa nkhondo yanu? Sindine Mfilisti kodi, ndi inu anyamata a Sauli? mudzisankhire munthu, atsikire kwa ine.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17
Onani 1 Samueli 17:8 nkhani