1 Samueli 18:11 BL92

11 Ndipo Sauli anaponya mkondowo; pakuti anati, Ndidzapyoza Davide ndi kumphatikiza ndi khoma. Ndipo Davide analewa kawiri kucoka pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:11 nkhani