1 Samueli 18:13 BL92

13 Cifukwa cace Sauli anamcotsa kuti asakhale naye, namuika akhale mtsogoleri wace wa anthu cikwi cimodzi; ndipo iye anatsogolera anthu kuturuka ndi kubwera nao.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:13 nkhani