1 Samueli 19:10 BL92

10 Ndipo Sauli anayesa kupyoza Davide kumphatikiza kukhoma ndi mkondowo; koma iye anadzilanditsa kucoka pamaso pa Sauli; ndipo analasa khoma; ndipo Davide anathawa napulumuka usiku uja.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:10 nkhani