1 Samueli 19:11 BL92

11 Ndipo Sauli anatumiza mithenga ku nyumba ya Davide imdikire, ndi kumupha m'mawa; koma Mikala mkazi wa Davide anamuuza, nati, Ukapanda kupulumutsa moyo wako usiku uno, udzaphedwa ndithu m'mawa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:11 nkhani