17 Nati Sauli kwa Mikala, Wandinyengeranii comweci, ndi kulola mdani wanga apulumuke? Ndipo Mikala anayankha Sauli, iye anati kwa ine, Undilole ndipite, ndingakuphe.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19
Onani 1 Samueli 19:17 nkhani