1 Samueli 19:18 BL92

18 Comweco anathawa Davide, napulumuka, nafika kwa Samueli: ku Rama, namuuza zonse Sauli anamcitira. Ndipo iye ndi Samueli anakhala ku Nayoti.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:18 nkhani