1 Samueli 19:20 BL92

20 Ndipo Sauli anatumiza mithenga kuti igwire Davide, ndipo pamene inaona gulu la aneneri alikunenera, ndi Samueli mkuru wao alikuimapo, mzimu wa Mulungu unagwera-mithenga ya Sauli, ninenera iyonso.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:20 nkhani