21 Ndipo pamene anauza Sauli, iye anatumiza mithenga yina; koma iyonso inanenera. Ndipo Sauli anatumiza mithenga kacitatu, nayonso inanenera.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19
Onani 1 Samueli 19:21 nkhani