1 Samueli 2:16 BL92

16 Ndipo ngati munthu akanena naye, Koma adzatentha mafuta tsopano apa, atatha, utenge monga mtima wako ufuna; uyo akanena naye, lai, koma undipatsire iyo tsopanoli, ukapanda kutero ndidzailanda.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:16 nkhani