1 Samueli 2:19 BL92

19 Ndiponso amace akamsokera mwinjiro waung'ono, nabwera nao kwa iye caka ndi caka, pakudza pamodzi ndi mwamuna wace kudzapereka nsembe ya pacaka.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:19 nkhani