1 Samueli 2:20 BL92

20 Ndipo Eli anadalitsa Elikana ndi mkazi wace, nati, Yehova akupatse mbeu ndi mkazi uyu m'malo mwa iye amene munampempha kwa Yehova. Ndipo iwowa anabwera kwao.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:20 nkhani