1 Samueli 2:21 BL92

21 Ndipo Yehova anakumbukila Hana, naima iye, nabala ana amuna atatu, ndi ana akazi awiri. Ndipo mwanayo Samueli anakula pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:21 nkhani