1 Samueli 2:33 BL92

33 Ndipo munthu wako, amene ndidzamleka osamlikha pa guwa langa, adzatha maso ako, ndi kumvetsa mtima wako cisoni; ndipo obadwa onse a m'banja lako adzamwalira akali biriwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:33 nkhani