1 Samueli 2:34 BL92

34 Ndipo ici cimene cidzafikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinehasi, cidzakhala cizindikilo kwa iwo, tsiku limodzi adzafa iwo onse awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:34 nkhani