1 Samueli 2:35 BL92

35 Ndipo ndidzadziukitsira wansembe wokhulupirika, amene adzacita monga cimene ciri mumtima mwanga ndi m'cifuniro canga; ndipo ndidzammangira nyumba yokhazikika, ndipo iyeyu adzayenda pamaso pa wodzozedwa wanga masiku onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:35 nkhani