1 Samueli 20:30 BL92

30 Pamenepo Sauli anapsa mtima ndi Jonatani, nanena naye, Iwe mwana wa mkazi wa matsutso ndi wopikisana, sindidziwa kodi kuti wasankha mwana wa Jeseyo kudzinyaza wekha, ndi usiwa wa mai wako yemwe?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:30 nkhani