1 Samueli 20:5 BL92

5 Nati Davide kwa Jonatani, Onani, mawa mwezi ukhala, ndipo ine ndiyenera kupita kukadya kwa mfumu, wosatsala; koma undilole ndikabisale kuthengo, kufikira tsiku lacitatu madzulo ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:5 nkhani