1 Samueli 20:6 BL92

6 Atate wako akandifuna pang'ono ponse, unene kuti, Davide anandiumirira ndimlole athamangire kwao ku Betelehemu, pakuti kumeneko kuli nsembe ya pacaka ya banja lao lonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:6 nkhani