1 Samueli 20:7 BL92

7 Tsono akati, Cabwino; kapolo wako adzakhala ndi mtendere; koma akapsa mtima, uzindikirepo kuti anatsimikiza mtima kundicitira coipa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:7 nkhani