1 Samueli 21:6 BL92

6 Comweco wansembeyo anampatsa mkate wopatulika, popeza panalibe mkate wina, koma mkate woonekera, umene adaucotsa pamaso pa Yehova, kuti akaike mkate wotentha tsiku lomwelo anacotsa winawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:6 nkhani