1 Samueli 21:7 BL92

7 Tsono munthu wina wa anyamata a Sauli anali komweko, tsiku lija, anacedwetsedwa pamaso pa Yehova; dzina lace ndiye Doegi wa ku Edomu, kapitao wa abusa a Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:7 nkhani