1 Samueli 22:6 BL92

6 Pakumva Sauli kuti anadziwika Davide, ndi anthu ace akukhala naye, Sauti analikukhala m'Gibeya, patsinde pa mtengo wa kumsanje, m'dzanja lace munali mkondo wace, ndi anyamata ace onse anaimirira pali iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:6 nkhani