1 Samueli 22:7 BL92

7 Ndipo Sauli anati kwa anyamata ace akuima comzinga, Imvani tsopano, inu a Benjamini; kodi mwana wa Jese adzakupatsani inu nonse minda, ndi minda yamphesa, kodi adzakuikani mukhale atsogoleri a zikwi ndi a mazana;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:7 nkhani